Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 M’makalatawo mfumu inalola Ayuda amene anali m’mizinda yosiyanasiyana kuti asonkhane+ ndi kuteteza miyoyo yawo. Inawalolanso kuwononga, kupha ndi kufafaniza magulu onse ankhondo a anthu+ ndi zigawo zimene zinali kuwachitira nkhanza, ngakhalenso ana ndi akazi ndiponso kufunkha zinthu zawo.+

  • Esitere 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ayuda ena onse amene anali m’zigawo+ za mfumu anasonkhana pamodzi kuti ateteze miyoyo yawo.+ Ndipo anabwezera+ adani awo ndi kupha anthu 75,000 amene anali kudana nawo, koma sanafunkhe zinthu zawo

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena