Salimo 118:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’mahema+ a olungama+Mumamveka mfuu yachisangalalo ndipo muli chipulumutso.+Dzanja lamanja la Yehova limachita zamphamvu.+ Salimo 145:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo adzalankhula mosefukira za kuchuluka kwa ubwino wanu,+Ndipo adzafuula mokondwera chifukwa cha chilungamo chanu.+ Yesaya 65:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atumiki anga adzafuula mokondwa chifukwa chokhala ndi chimwemwe mumtima,+ koma inuyo mudzalira chifukwa chopwetekedwa mtima ndipo mudzafuula chifukwa chosweka mtima.+
15 M’mahema+ a olungama+Mumamveka mfuu yachisangalalo ndipo muli chipulumutso.+Dzanja lamanja la Yehova limachita zamphamvu.+
7 Iwo adzalankhula mosefukira za kuchuluka kwa ubwino wanu,+Ndipo adzafuula mokondwera chifukwa cha chilungamo chanu.+
14 Atumiki anga adzafuula mokondwa chifukwa chokhala ndi chimwemwe mumtima,+ koma inuyo mudzalira chifukwa chopwetekedwa mtima ndipo mudzafuula chifukwa chosweka mtima.+