Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “‘Tsopano munthu+ akaona wina akuchita tchimo, kapena wamva kuti wina wachita tchimo,+ munthu ameneyo ndi mboni. Akamva chilengezo* kuti akachitire umboni za wochimwayo koma iye osapita kukanena,+ ndiye kuti wachimwa. Ayenera kuyankha mlandu wa cholakwa chakecho.

  • Esitere 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 M’bukumo anapeza kuti mwalembedwa zimene Moredekai anaulula+ zokhudza Bigitana ndi Teresi, nduna ziwiri+ za panyumba ya mfumu, alonda apakhomo, amene anafuna kupha Mfumu Ahasiwero.

  • Miyambo 29:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Wochita ubwenzi ndi mbala akudana ndi moyo wake.+ Iye angamve lumbiro lokhudza temberero, koma osakanena chilichonse.+

  • Ezekieli 33:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Koma iwe mwana wa munthu, ine ndakuika kuti ukhale mlonda wa nyumba ya Isiraeli.+ Umve mawu ochokera pakamwa panga ndi kundichenjezera anthuwo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena