2 Samueli 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako anaika mdima momuzungulira ngati misasa,+Anaika madzi akuda ndi mtambo wakuda.+