Yobu 37:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amakuchititsa kumveka pansi ponse pa thambo,Ndipo mphezi yake+ imafika kumalekezero a dziko lapansi. Mateyu 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti mmene mphezi+ imang’animira kuchokera kum’mawa, ndi kuwala mpaka kumadzulo, zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo kwa Mwana wa munthu.+
3 Amakuchititsa kumveka pansi ponse pa thambo,Ndipo mphezi yake+ imafika kumalekezero a dziko lapansi.
27 Pakuti mmene mphezi+ imang’animira kuchokera kum’mawa, ndi kuwala mpaka kumadzulo, zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo kwa Mwana wa munthu.+