Salimo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?+N’chifukwa chiyani mukuchedwa kundipulumutsa?+N’chifukwa chiyani simukumva mawu a kubuula kwanga?+ Salimo 38:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndalefuka ndipo ndaponderezeka kwambiri.Ndikulira mofuula chifukwa cha kuvutika kwa mtima wanga.+ Yesaya 59:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tonsefe tikungolira ngati zimbalangondo ndipo tikungokhalira kubuula momvetsa chisoni ngati njiwa.+ Tinali kuyembekezera chilungamo+ koma sichinabwere. Tinali kuyembekezera chipulumutso koma chakhala nafe kutali.+
22 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?+N’chifukwa chiyani mukuchedwa kundipulumutsa?+N’chifukwa chiyani simukumva mawu a kubuula kwanga?+
11 Tonsefe tikungolira ngati zimbalangondo ndipo tikungokhalira kubuula momvetsa chisoni ngati njiwa.+ Tinali kuyembekezera chilungamo+ koma sichinabwere. Tinali kuyembekezera chipulumutso koma chakhala nafe kutali.+