Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 29:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola,+ ulemerero,+ ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi za padziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu+ ndi wanu, inu Yehova, ndinunso Wokwezeka monga mutu pa onse.+

  • Yobu 36:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mulungutu amachita zinthu zapamwamba ndi mphamvu zake.

      Kodi mphunzitsi winanso ndani wofanana naye?

  • Yesaya 40:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Kwezani maso anu kumwamba muone. Kodi ndani amene analenga zinthu zimenezo?+ Ndi amene akutsogolera gulu lonse la nyenyezizo malinga ndi chiwerengero chake, ndipo amaziitana potchula iliyonse dzina lake.+ Chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake zoopsa,+ ndiponso chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zambiri zochitira zinthu, palibe imene imasowa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena