Salimo 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikayang’ana kumwamba, ntchito ya zala zanu,+Mwezi ndi nyenyezi zimene munapanga,+ Salimo 102:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munaika kalekale maziko a dziko lapansi,+Ndipo kumwamba ndiko ntchito ya manja anu.+
3 Ndikayang’ana kumwamba, ntchito ya zala zanu,+Mwezi ndi nyenyezi zimene munapanga,+ Salimo 102:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munaika kalekale maziko a dziko lapansi,+Ndipo kumwamba ndiko ntchito ya manja anu.+