Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno Mulungu anatcha kuwalako Usana,+ koma mdimawo anautcha Usiku.+ Panali madzulo ndiponso panali m’mawa, tsiku loyamba.

  • Salimo 74:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Usana ndi wanu, usikunso ndi wanu.+

      Inu munapanga chounikira, munapanga dzuwa.+

  • Salimo 148:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Zonsezi zitamande dzina la Yehova,+

      Pakuti iye analamula ndipo zinalengedwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena