Yobu 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mpweya wa Mulungu umapereka madzi oundana,+Ndipo malo aakulu a madzi ndi oundana.+