Salimo 104:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mkango wamphamvu umabangula pofunafuna nyama,+Ndiponso popempha chakudya kwa Mulungu.+ Salimo 145:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zolengedwa zonse zimayang’ana kwa inu mwachiyembekezo,+Ndipo mumazipatsa chakudya pa nyengo yake.+ Nahumu 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mkango unali kukhadzulakhadzula nyama yokwanira kuti udyetse ana ake ndipo unali kupha nyama kuti upatse mikango yaikazi. Mapanga ake anali kukhala odzaza ndi nyama, ndipo malo ake obisalamo anali ndi nyama zokhadzulakhadzula.+
15 Zolengedwa zonse zimayang’ana kwa inu mwachiyembekezo,+Ndipo mumazipatsa chakudya pa nyengo yake.+
12 Mkango unali kukhadzulakhadzula nyama yokwanira kuti udyetse ana ake ndipo unali kupha nyama kuti upatse mikango yaikazi. Mapanga ake anali kukhala odzaza ndi nyama, ndipo malo ake obisalamo anali ndi nyama zokhadzulakhadzula.+