Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 5:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pamenepo ziboda za mahatchi* zinaguguda pansi,+

      Chifukwa cha kuthamangathamanga kwa mahatchiwo.

  • Salimo 32:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Anthu inu, musakhale ngati hatchi kapena nyulu* yosazindikira,+

      Imene munthu amachita kuimanga chingwe chapakamwa ndi chapamutu kuti athetse kupulupudza kwake,+

      Ndi kuti aiyandikire.”+

  • Yeremiya 47:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Abambo adzathawa osayang’ana m’mbuyo kuti apulumutse ana awo. Adzachita izi chifukwa chakuti sadzalimba mtima pakumva mgugu wa mahatchi ake,+ phokoso la magaleta ake ankhondo+ ndi kulira kwa mawilo ake.+

  • Habakuku 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mahatchi* ake ndi aliwiro kuposa akambuku* ndiponso ndi oopsa kuposa mimbulu yoyenda usiku.+ Mahatchi ake ankhondo amachita mgugu ndipo amachokera kutali. Mahatchiwo amauluka ngati chiwombankhanga chimene chikuthamangira chakudya chake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena