Deuteronomo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mose anamwalira ali ndi zaka 120.+ Diso lake silinachite mdima+ ndipo anali adakali ndi mphamvu.+