Miyambo 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+ Miyambo 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mawu olankhulidwa pa nthawi yoyenera ali ngati zipatso za maapozi agolide m’mbale zasiliva.+
18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+