-
Yobu 31:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ngati ndili pachipata ndinaonapo mwana wamasiye akufunika thandizo langa,+
Koma ine n’kumuopseza ndi dzanja langa,+
-
Malaki 3:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 “Anthu inu ndidzakuyandikirani kuti ndikuweruzeni.+ Sindidzazengereza kupereka umboni+ wotsutsa amatsenga,+ achigololo,+ olumbira monama+ komanso ochita chinyengo pa malipiro a munthu waganyu.+ Sindidzazengereza kupereka umboni wotsutsa anthu ochitira chinyengo mkazi wamasiye,+ mwana wamasiye*+ ndiponso opondereza alendo.+ Anthu amenewa sakundiopa,”+ watero Yehova wa makamu.
-
-
-