Yobu 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komabe, amuna nonsenu mungathe kuyambiranso kundinena. Chotero pitirizani,Chifukwa sindikuonapo wanzeru pakati panu.+
10 Komabe, amuna nonsenu mungathe kuyambiranso kundinena. Chotero pitirizani,Chifukwa sindikuonapo wanzeru pakati panu.+