Yobu 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chonde sinthani maganizo anu, kuti pachitike chilungamo.Ndithu sinthani maganizo. Inetu ndikadali wolungama.+ Aroma 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngakhale anali kunena motsimikiza kuti ndi anzeru, iwo anakhala opusa+
29 Chonde sinthani maganizo anu, kuti pachitike chilungamo.Ndithu sinthani maganizo. Inetu ndikadali wolungama.+