Deuteronomo 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 musamvere mawu a mneneriyo kapena wolotayo,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu akukuyesani+ kuti adziwe ngati mukukonda Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse.+ Yobu 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti iye amadziwa bwino njira imene ine ndimadutsa.+Akamaliza kundiyesa, ndidzakhala ngati golide.+ Salimo 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chonde, thetsani kuipa kwa anthu oipa,+Ndipo khazikitsani wolungama.+Mulungu pokhala wolungama+ akuyesa mtima+ ndi impso.+
3 musamvere mawu a mneneriyo kapena wolotayo,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu akukuyesani+ kuti adziwe ngati mukukonda Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse.+
10 Pakuti iye amadziwa bwino njira imene ine ndimadutsa.+Akamaliza kundiyesa, ndidzakhala ngati golide.+
9 Chonde, thetsani kuipa kwa anthu oipa,+Ndipo khazikitsani wolungama.+Mulungu pokhala wolungama+ akuyesa mtima+ ndi impso.+