Yobu 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzandiyeza pasikelo zolondola,+Ndipo Mulungu adzadziwa kuti ndili ndi mtima wosagawanika.+ Salimo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwasanthula mtima wanga, mwandifufuza usiku,+Ndipo mwandiyenga. Mudzaona kuti sindinaganizire kuchita choipa chilichonse.+Pakamwa panga sipadzaphwanya malamulo.+ 1 Petulo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zimenezi zikukuchitikirani kuti chikhulupiriro chanu, chimene chayesedwa+ ndipo n’chamtengo wapatali kuposa golide amene amawonongekabe ngakhale kuti anadutsa m’moto,+ chidzakuchititseni kutamandidwa ndiponso kulandira ulemerero ndi ulemu, zochita za Yesu Khristu zikadzaululika.*+
3 Mwasanthula mtima wanga, mwandifufuza usiku,+Ndipo mwandiyenga. Mudzaona kuti sindinaganizire kuchita choipa chilichonse.+Pakamwa panga sipadzaphwanya malamulo.+
7 Zimenezi zikukuchitikirani kuti chikhulupiriro chanu, chimene chayesedwa+ ndipo n’chamtengo wapatali kuposa golide amene amawonongekabe ngakhale kuti anadutsa m’moto,+ chidzakuchititseni kutamandidwa ndiponso kulandira ulemerero ndi ulemu, zochita za Yesu Khristu zikadzaululika.*+