Yesaya 33:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Palibe munthu wokhala m’dzikolo amene adzanene kuti: “Ndikudwala.”+ Anthu okhala mmenemo adzakhala amene machimo awo anakhululukidwa.+
24 Palibe munthu wokhala m’dzikolo amene adzanene kuti: “Ndikudwala.”+ Anthu okhala mmenemo adzakhala amene machimo awo anakhululukidwa.+