Genesis 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Simungachite zimenezo, kupha munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama aone zofanana ndi woipa.+ Simungachite zimenezo ayi.+ Kodi Woweruza wa dziko lonse lapansi sadzachita cholungama?”+ Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ Aroma 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndilekeranji kunena zimene amatinamizira zija,+ ndiponso zimene ena amati timanena zakuti: “Tiyeni tichite zoipa kuti pakhale zinthu zabwino”?+ Chiweruzo+ chowafikira anthu amenewo n’chogwirizana ndi chilungamo.+
25 Simungachite zimenezo, kupha munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama aone zofanana ndi woipa.+ Simungachite zimenezo ayi.+ Kodi Woweruza wa dziko lonse lapansi sadzachita cholungama?”+
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
8 Ndilekeranji kunena zimene amatinamizira zija,+ ndiponso zimene ena amati timanena zakuti: “Tiyeni tichite zoipa kuti pakhale zinthu zabwino”?+ Chiweruzo+ chowafikira anthu amenewo n’chogwirizana ndi chilungamo.+