Yobu 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chonde sinthani maganizo anu, kuti pachitike chilungamo.Ndithu sinthani maganizo. Inetu ndikadali wolungama.+ Yobu 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chonsecho mukudziwa kuti ndine wosalakwa,+Ndipo palibe wondipulumutsa m’manja mwanu.+
29 Chonde sinthani maganizo anu, kuti pachitike chilungamo.Ndithu sinthani maganizo. Inetu ndikadali wolungama.+