Yobu 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye amene chidaliro chake chimatha,Amene amadalira ulusi* wa kangaude.+ Yobu 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zinthu zimene amazidalira zidzachotsedwa m’hema wake,+Ndipo zidzapita naye kwa mfumu ya zoopsa.