Yobu 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zimene amuna inu mukuzidziwa, inenso ndikuzidziwa bwino.Si ine wotsika kwa inu.+ Miyambo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nzeru zikalowa mumtima mwako,+ ndipo kudziwa zinthu kukakhala kosangalatsa m’moyo wako,+