Yobu 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inenso ndili ndi zolinga zabwino+ ngati inuyo.Si ine wonyozeka kwa inu,+Ndipo ndani amene alibe zinthu ngati zimenezi? 2 Akorinto 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndikuona kuti sindikuchepa+ mwanjira ina iliyonse kwa atumwi anu apamwambawo.+
3 Inenso ndili ndi zolinga zabwino+ ngati inuyo.Si ine wonyozeka kwa inu,+Ndipo ndani amene alibe zinthu ngati zimenezi?