Yobu 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nanga kuli bwanji anthu okhala m’nyumba zadothi,Amene maziko awo ali m’fumbi?+Iwo amathudzulidwa mosavuta kuposa kadziwotche.
19 Nanga kuli bwanji anthu okhala m’nyumba zadothi,Amene maziko awo ali m’fumbi?+Iwo amathudzulidwa mosavuta kuposa kadziwotche.