Yobu 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kwa Mulungu woona, ine ndili ngati inu nomwe.+Inenso ndinaumbidwa ndi dongo.+ Yesaya 50:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amene adzanene kuti ndine wolungama ali pafupi.+ Ndani angalimbane nane? Tiyeni tikaonane pabwalo lamilandu.+ Kodi wotsutsana nane pa mlandu ndani?+ Abwere kufupi.+
8 Amene adzanene kuti ndine wolungama ali pafupi.+ Ndani angalimbane nane? Tiyeni tikaonane pabwalo lamilandu.+ Kodi wotsutsana nane pa mlandu ndani?+ Abwere kufupi.+