Genesis 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako, Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kufumbi lapansi,+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ m’mphuno mwake, munthuyo n’kukhala wamoyo.+ Yobu 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chonde kumbukirani kuti munandiumba ndi dongo,+Ndipo mudzandibwezera kufumbi.+ 1 Akorinto 15:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Munthu woyambayo anachokera padziko lapansi ndipo anapangidwa ndi fumbi.+ Wachiwiriyo anachokera kumwamba.+ 2 Akorinto 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komabe, tili ndi chuma+ chimenechi m’zonyamulira+ zoumbidwa ndi dothi,+ kuti mphamvu+ yoposa yachibadwa ichokere kwa Mulungu,+ osati kwa ife.+
7 Kenako, Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kufumbi lapansi,+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ m’mphuno mwake, munthuyo n’kukhala wamoyo.+
47 Munthu woyambayo anachokera padziko lapansi ndipo anapangidwa ndi fumbi.+ Wachiwiriyo anachokera kumwamba.+
7 Komabe, tili ndi chuma+ chimenechi m’zonyamulira+ zoumbidwa ndi dothi,+ kuti mphamvu+ yoposa yachibadwa ichokere kwa Mulungu,+ osati kwa ife.+