Salimo 51:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani! Anandilandira mu zowawa za pobereka ndili wochimwa.+Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+ 1 Akorinto 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti monga mkazi ali wochokera kwa mwamuna,+ mwamunanso amakhalapo kudzera mwa mkazi,+ koma zinthu zonse ndi zochokera kwa Mulungu.+
5 Taonani! Anandilandira mu zowawa za pobereka ndili wochimwa.+Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+
12 Pakuti monga mkazi ali wochokera kwa mwamuna,+ mwamunanso amakhalapo kudzera mwa mkazi,+ koma zinthu zonse ndi zochokera kwa Mulungu.+