Genesis 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+ Genesis 47:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yakobo anayankha Farao kuti: “Zaka za moyo wanga monga mlendo m’malo osiyanasiyana zikukwana 130.+ Zaka zimenezi zakhala zowerengeka ndi zosautsa,+ ndipo sizinafike pa zaka za moyo wa makolo anga monga alendo m’malo osiyanasiyana.”+ Mlaliki 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Masiku ake onse, ntchito yakeyo imamubweretsera zowawa ndi zokhumudwitsa.+ Komanso usiku mtima wake sugona.+ Izinso n’zachabechabe.
19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+
9 Yakobo anayankha Farao kuti: “Zaka za moyo wanga monga mlendo m’malo osiyanasiyana zikukwana 130.+ Zaka zimenezi zakhala zowerengeka ndi zosautsa,+ ndipo sizinafike pa zaka za moyo wa makolo anga monga alendo m’malo osiyanasiyana.”+
23 Masiku ake onse, ntchito yakeyo imamubweretsera zowawa ndi zokhumudwitsa.+ Komanso usiku mtima wake sugona.+ Izinso n’zachabechabe.