Yesaya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthambi+ idzatuluka pachitsa cha Jese,+ ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzakhala yobereka zipatso.+ Danieli 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Popeza ananena kuti asiye chitsa cha mtengowo,+ inu mudzayambiranso kulamulira mu ufumu wanu mutadziwa kuti Mulungu ndiye akulamulira kumwamba.+ Danieli 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako, mphukira yochokera kumizu+ yake idzauka ndi kulowa m’malo mwake* ndipo idzafika kwa gulu lankhondo ndi kuukira mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri wa mfumu ya kumpoto, moti mphukirayo idzawathira nkhondo ndi kupambana.
11 Nthambi+ idzatuluka pachitsa cha Jese,+ ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzakhala yobereka zipatso.+
26 “‘Popeza ananena kuti asiye chitsa cha mtengowo,+ inu mudzayambiranso kulamulira mu ufumu wanu mutadziwa kuti Mulungu ndiye akulamulira kumwamba.+
7 Kenako, mphukira yochokera kumizu+ yake idzauka ndi kulowa m’malo mwake* ndipo idzafika kwa gulu lankhondo ndi kuukira mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri wa mfumu ya kumpoto, moti mphukirayo idzawathira nkhondo ndi kupambana.