Salimo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munthu ameneyo adzakhala ngati mtengo wobzalidwa m’mphepete mwa mitsinje ya madzi,+Umene umabala zipatso m’nyengo yake,+Umenenso masamba ake safota,+Ndipo zochita zake zonse zidzamuyendera bwino.+
3 Munthu ameneyo adzakhala ngati mtengo wobzalidwa m’mphepete mwa mitsinje ya madzi,+Umene umabala zipatso m’nyengo yake,+Umenenso masamba ake safota,+Ndipo zochita zake zonse zidzamuyendera bwino.+