Danieli 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Ndiyeno iwe pita ku mapeto+ ndipo udzapuma.+ Koma udzauka kuti ulandire gawo lako pa mapeto a masikuwo.”+ Yohane 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa idzafika nthawi pamene onse ali m’manda achikumbutso+ adzamva mawu ake Yohane 11:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Atanena zimenezi, anafuula mokweza mawu kuti: “Lazaro, tuluka!”+
13 “Ndiyeno iwe pita ku mapeto+ ndipo udzapuma.+ Koma udzauka kuti ulandire gawo lako pa mapeto a masikuwo.”+
28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa idzafika nthawi pamene onse ali m’manda achikumbutso+ adzamva mawu ake