Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 45:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ana anu adzatenga+ malo a makolo anu,+

      Ndipo mudzawaika kukhala akalonga padziko lonse lapansi.+

  • Yohane 11:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Marita anati: “Ndikudziwa kuti adzauka pa kuuka kwa akufa+ m’tsiku lomaliza.”

  • Machitidwe 17:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”

  • Machitidwe 24:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndipo ine ndili ndi chiyembekezo+ mwa Mulungu, chimenenso anthu awa ali nacho, kuti kudzakhala kuuka+ kwa olungama+ ndi osalungama omwe.+

  • Chivumbulutso 20:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiye ndinaona akufa, olemekezeka ndi onyozeka,+ ataimirira pamaso pa mpando wachifumuwo, ndipo mipukutu inafunyululidwa. Koma mpukutu wina unafunyululidwa, ndiwo mpukutu wa moyo.+ Ndipo akufa anaweruzidwa malinga ndi zolembedwa m’mipukutuyo, mogwirizana ndi ntchito zawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena