Aroma 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pakuti “ndani akudziwa maganizo a Yehova,+ kapena ndani angakhale phungu wake?”+ 1 Akorinto 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi ndi munthu uti amene angadziwe za munthu kupatulapo mzimu+ umene uli mwa munthuyo? Momwemonso, palibe amene akudziwa zinthu za Mulungu, kupatulapo mzimu+ wa Mulungu.
11 Kodi ndi munthu uti amene angadziwe za munthu kupatulapo mzimu+ umene uli mwa munthuyo? Momwemonso, palibe amene akudziwa zinthu za Mulungu, kupatulapo mzimu+ wa Mulungu.