Yobu 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zimene amuna inu mukuzidziwa, inenso ndikuzidziwa bwino.Si ine wotsika kwa inu.+ Yobu 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndamva zinthu zambiri ngati zimenezi.Nonsenu ndinu otonthoza onditopetsa!+