Salimo 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Taonani! Wina ali ndi pakati pa zinthu zoipa,+Watenga pakati pa mavuto ndipo ndithu adzabereka chinyengo.+ Yesaya 59:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Palibe amene akufuula mwachilungamo,+ ndipo palibe amene amalankhula mokhulupirika akapita kukhoti. Anthu inu mukukhulupirira zinthu zachabechabe+ ndipo mukulankhula zopanda pake.+ Mwatenga pakati pa mavuto ndipo mwabereka zopweteka.+ Yakobo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiye chilakolako chikatenga pakati, chimabala tchimo.+ Nalonso tchimo likakwaniritsidwa, limabweretsa imfa.+
14 Taonani! Wina ali ndi pakati pa zinthu zoipa,+Watenga pakati pa mavuto ndipo ndithu adzabereka chinyengo.+
4 Palibe amene akufuula mwachilungamo,+ ndipo palibe amene amalankhula mokhulupirika akapita kukhoti. Anthu inu mukukhulupirira zinthu zachabechabe+ ndipo mukulankhula zopanda pake.+ Mwatenga pakati pa mavuto ndipo mwabereka zopweteka.+
15 Ndiye chilakolako chikatenga pakati, chimabala tchimo.+ Nalonso tchimo likakwaniritsidwa, limabweretsa imfa.+