Genesis 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Mulungu anati: “N’chiyani chimene wachitachi? Tamvera tsono. Magazi a m’bale wako akundilirira munthaka.+ Salimo 72:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Adzawombola miyoyo yawo ku chipsinjo ndi chiwawa,Ndipo adzaona magazi awo kukhala amtengo wapatali.+
10 Pamenepo Mulungu anati: “N’chiyani chimene wachitachi? Tamvera tsono. Magazi a m’bale wako akundilirira munthaka.+
14 Adzawombola miyoyo yawo ku chipsinjo ndi chiwawa,Ndipo adzaona magazi awo kukhala amtengo wapatali.+