Yobu 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Woipayo amamva phokoso la zoopsa m’makutu ake,Pa nthawi yamtendere wolanda amam’bwerera.+ Yobu 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Muvi udzatulukira kumsana kwake,Ndipo chida chonyezimira chidzaboola ndulu yake.+Zida zoopsa zidzam’pweteka.+
25 Muvi udzatulukira kumsana kwake,Ndipo chida chonyezimira chidzaboola ndulu yake.+Zida zoopsa zidzam’pweteka.+