Salimo 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Mulungu wanga, ine ndimaitana usana koma simundiyankha.+Usiku ndimaitanabe, moti sindikukhala chete.+ Habakuku 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Inu Yehova, kodi ndidzalirira thandizo koma inu osandimva kufikira liti?+ Kodi ndidzapempha thandizo kuti mundipulumutse ku chiwawa koma inu osandimva kufikira liti?+
2 Inu Mulungu wanga, ine ndimaitana usana koma simundiyankha.+Usiku ndimaitanabe, moti sindikukhala chete.+
2 “Inu Yehova, kodi ndidzalirira thandizo koma inu osandimva kufikira liti?+ Kodi ndidzapempha thandizo kuti mundipulumutse ku chiwawa koma inu osandimva kufikira liti?+