Yobu 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 N’chifukwa chiyani mukubisa nkhope yanu,+N’kunditenga ine ngati mdani wanu?+