Yobu 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo ayasamula kukamwa kwawo kuti andimeze.+Andimenya mbama ndi mnyozo.Asonkhana ambirimbiri kuti alimbane nane.+ Yobu 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anzanga asanduka ondilankhulira otsutsana nane.+Diso langa lakhala likuyang’ana kwa Mulungu osagona.+ Yobu 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndithu, onyoza andizungulira,+Ndipo diso langa likuyang’anitsitsa khalidwe lawo lopanduka. Aheberi 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ena analandira mayesero awo mwa kutonzedwa ndi kukwapulidwa, komanso kuposa pamenepo, mwa maunyolo+ ndi ndende.+
10 Iwo ayasamula kukamwa kwawo kuti andimeze.+Andimenya mbama ndi mnyozo.Asonkhana ambirimbiri kuti alimbane nane.+
20 Anzanga asanduka ondilankhulira otsutsana nane.+Diso langa lakhala likuyang’ana kwa Mulungu osagona.+
36 Ena analandira mayesero awo mwa kutonzedwa ndi kukwapulidwa, komanso kuposa pamenepo, mwa maunyolo+ ndi ndende.+