Yobu 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chonsecho iye wadzaza nyumba zawo ndi zinthu zabwino,+Ndipo malangizo a anthu oipa ali kutali ndi ine.+ Salimo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Wodala+ ndi munthu amene sayenda motsatira malangizo a anthu oipa,+Saima m’njira ya anthu ochimwa,+Ndipo sakhala pansi pamodzi ndi anthu onyoza.+
18 Chonsecho iye wadzaza nyumba zawo ndi zinthu zabwino,+Ndipo malangizo a anthu oipa ali kutali ndi ine.+
1 Wodala+ ndi munthu amene sayenda motsatira malangizo a anthu oipa,+Saima m’njira ya anthu ochimwa,+Ndipo sakhala pansi pamodzi ndi anthu onyoza.+