Yobu 42:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova atanena mawu amenewa kwa Yobu, Yehovayo anauza Elifazi wa ku Temani kuti:“Mkwiyo wanga wayakira iweyo ndi anzako awiriwo+ chifukwa inu simunanene zoona za ine,+ monga wachitira Yobu mtumiki wanga. Miyambo 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mtsogoleri akamamvera mabodza, onse omutumikira adzakhala oipa.+ Miyambo 31:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kukamazizira, iye sadera nkhawa za banja lake chifukwa a m’banja lake onse amavala zovala zotentha.*+
7 Yehova atanena mawu amenewa kwa Yobu, Yehovayo anauza Elifazi wa ku Temani kuti:“Mkwiyo wanga wayakira iweyo ndi anzako awiriwo+ chifukwa inu simunanene zoona za ine,+ monga wachitira Yobu mtumiki wanga.
21 Kukamazizira, iye sadera nkhawa za banja lake chifukwa a m’banja lake onse amavala zovala zotentha.*+