Yesaya 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’masiku anu, kukhulupirika kudzabweretsa chipulumutso chachikulu.+ Nazonso nzeru, kudziwa zinthu,+ ndi kuopa Yehova,+ komwe ndiko chuma chake zidzabweretsa chipulumutso chachikulu.
6 M’masiku anu, kukhulupirika kudzabweretsa chipulumutso chachikulu.+ Nazonso nzeru, kudziwa zinthu,+ ndi kuopa Yehova,+ komwe ndiko chuma chake zidzabweretsa chipulumutso chachikulu.