Salimo 37:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komanso sangalala mwa Yehova,+Ndipo adzakupatsa zokhumba za mtima wako.+