Salimo 116:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa Yehova,+Pamaso pa anthu ake onse. Mlaliki 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa palibe amene amasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+
4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa palibe amene amasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+