Genesis 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamene iye anali kuzengereza,+ alendowo, mwa chifundo cha Yehova pa iye,+ anagwira dzanja iyeyo, mkazi wake, ndi ana ake aakazi awiriwo, n’kuwatulutsa kukawasiya kunja kwa mzinda.+ 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+
16 Pamene iye anali kuzengereza,+ alendowo, mwa chifundo cha Yehova pa iye,+ anagwira dzanja iyeyo, mkazi wake, ndi ana ake aakazi awiriwo, n’kuwatulutsa kukawasiya kunja kwa mzinda.+
9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+