Salimo 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti iye sananyoze,+Kapena kunyansidwa ndi nsautso ya munthu wosautsidwa.+Ndipo sanam’bisire nkhope yake.+Pamene anamulirira kuti amuthandize, iye anamva.+ Yesaya 57:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti ine sindidzatsutsana nanu mpaka kalekale, ndiponso sindidzakhala wokwiya mpaka kalekale.+ Popeza chifukwa cha ine, mzimu wa munthu ukhoza kufooka,+ ngakhalenso zinthu zopuma zimene ineyo ndinapanga.+
24 Pakuti iye sananyoze,+Kapena kunyansidwa ndi nsautso ya munthu wosautsidwa.+Ndipo sanam’bisire nkhope yake.+Pamene anamulirira kuti amuthandize, iye anamva.+
16 Pakuti ine sindidzatsutsana nanu mpaka kalekale, ndiponso sindidzakhala wokwiya mpaka kalekale.+ Popeza chifukwa cha ine, mzimu wa munthu ukhoza kufooka,+ ngakhalenso zinthu zopuma zimene ineyo ndinapanga.+