Salimo 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti ndasunga njira za Yehova,+Sindinachoke kwa Mulungu wanga. Ndikanatero, ndikanachita chinthu choipa.+ Salimo 44:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mitima yathu sinakhale yosakhulupirika n’kuchoka panjira yanu,+Ndipo mapazi athu sanapatuke panjira yanu.+
21 Pakuti ndasunga njira za Yehova,+Sindinachoke kwa Mulungu wanga. Ndikanatero, ndikanachita chinthu choipa.+
18 Mitima yathu sinakhale yosakhulupirika n’kuchoka panjira yanu,+Ndipo mapazi athu sanapatuke panjira yanu.+